Books tagged: christianity in malawi

These results show books which have been specifically tagged with this keyword. You can also try doing a general search for the term "christianity in malawi" .
You may also limit results to books that contain two tags.
Some content may be filtered out. To view such content, change your filtering option.

Found 18 results

Kukhululuka Kwaphweketsedwa
Price: $2.50 USD. Words: 4,470. Language: Chichewa. Published: August 12, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Relationships
"Ndipo pamene muimirira ndi kupemphera, khululukirani, ngati munthu wakulakwirani kanthu; kuti Atate wanunso ali Kumwamba akhululukire inu zolakwa zanu. Koma NGATI INU SIMUKHULULUKIRA, ATATE WANU WAKUMWAMBA SAZAKHULULUKIRA INU ZOLAKWA ZANU" (Marko 11:25-26). Kodi ndimezi zikukunjenjemeretsani? Yankho lanu lilipano. Mu bukhu lofunikirali, muphunzira kukhululukira mosavuta
Ena...
Price: $5.00 USD. Words: 12,220. Language: Chichewa. Published: August 12, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Inspirational
Baibulo limatilangiza ife ku: "Munthu yense asapenyerere zake za iye yekha, koma yense apenyererenso za mnzakeyo" (Afilipi 2:4). M'bukhu la m'nthawi yakeli, Dag Heward-Mills akukuwuzani inu mupitirire kuganiza za inu nokha ndi kuganizanso za ena! Mukondenso ena! Muganizirenso ena! Musamalenso za ena! Mukhalenso chifukwa cha ena! Yesu anadza kudzatifera ife chifukwa Iye anaganiza za "ena". Ine ndik
Wodzozedwa ndi Kudzoza Kwake
Price: $7.50 USD. Words: 22,300. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Inspirational
Chuma cha kudzodza chili mwa odzodzedwa. Kudzoza sikosiyanitsidwa ndi munthu wodzozedwa. Kudzoza kuli mwa munthu wa Mulungu! Kudzoza kuli ndi munthu wa Mulungu! Kudzoza kuli pa munthu wa Mulungu. Bukhu latsopano ndi losangalasa la Dag Heward-Mills lisangalasa mitima ya iwo omwe akufunafuna kudzoza.
Zomwe Zikutanthauza Kukhala Wa Nzeru Monga Njoka
Price: $12.50 USD. Words: 27,620. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Inspirational
Yesu anati: mukhale ochenjera ngati njoka ndi oona mtima ngati nkhunda. Kodi njoka ndizochenjeradi? Nchifukwa chiyani Yesu angapereke langizo ngati limeneli? Tengani kaulendo mu bukhu lopangitsa chidwiri la Dag Heward-Mills, ndi kuzipezera nzeru zobisika za njoka.
Luso la Kutsatira
Price: $10.00 USD. Words: 47,920. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Inspirational
Kutsatira Mulungu ndi ulendo wosangalatsa wopeza zinthu. Kutsatira ndi kutengera anthu ena ndi luso lachikale lophunzirira lomwe Yesu Khristu anasankha ngati njira yaikulu yophunzitsira. M’malo mochita manyazi ndi njira yoyesedwa ndi nthawiyi, ndi nthawi yomvetsetsa kukongola ndi kudzichepetsa kwa luso la kutsatira. Mu bukhuli, muzapeza yemwe, chomwe ndi momwe mungatsatire moyenerera. Bukhu lopamb
Mpingo Waukulu
Price: $10.00 USD. Words: 30,880. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Ministry / Pastoral Resources
“…Tuluka, nupite kumiseu ndi njira za kuminda, nuwaumirize anthu alowe. KUTI NYUMBA YANGA IDZALE.” Luka 14:23. Kulira kwa Mulungu ndi kwakuti dziko lonse lipulumutsidwe, ndi kuti nyumba Yake-tchalitchi-lidzale! Kuchokera ku vumbulutso limeneri bukhu iri linabwera., “Mpingo Waukulu” lolembedwa ndi Bishop Dag Heward-Mills, m’busa wa umodzi mwa mipingo yaikulu kwambiri ku Ghana. Mpingo wanu ndi utumi
Sinthani Utumiki Wanu Wa Ubusa
Price: $10.00 USD. Words: 29,330. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Ministry / Pastoral Resources
Iri ndi bukhu lolandiridwadi. Bishopu Dag Heward-Mills, m’busa iye mwini, akulongosola zifukwa ndi momwe ungapangire utumiki waubusa kuchita bwino.
Luso la Kumva
Price: $10.00 USD. Words: 33,130. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Spiritual Growth
Palibe mutu wofunikira kwambiri kuposa kukhala mu chifuniro cha Mulungu. Chokhacho chomwe chikasiyanitse azitumiki a uthenga ndi kuthekera kwawo kwa kumva mawu a Mulungu molondola. Momwe kulili kwabwino kutsatira Mzimu Woyera ku chifuniro cha Mulungu. Mukakhala mu chifuniro cha Mulungu, muzachita bwino ndipo muzakwaniritsa zokhumba zonse kwa Mulungu. Ntchito yapamwambayi yolembedwa ndi Dag Heward-
Iwo Amene Ali Odzikuza
Price: $8.00 USD. Words: 26,890. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Life / Inspirational
Kudzikweza ndi poizoni wakupha amene waononga mtundu wa anthu mzaka zambiri. Chifukwa nkosatheka, kudzikweza kumakwaniritsa kupangitsa chionongeko chachikulu popanda kuonekera. Tingamenyane bwanji ndi chiopsezo chimenechi ku miyoyo yathu? Ndi katemera wa kudzichepetsa! Kudzichepetsa ndi chabwino chauzimu. Ochepa akwanitsa kulemba zokhudzana ndi chofunikira chauzimuchi. Mu bukhu latsopano losangala
Luso la Ubusa
Price: $12.50 USD. Words: 44,100. Language: Chichewa. Published: June 13, 2019. Categories: Nonfiction » Religion & Spirituality » Christian Ministry / Pastoral Resources
Ngati ndinu m’busa wa nkhosa za Mulungu, muzathandizika kwambiri ndi ntchito yabwinoyi. Masamba amenewa ali ndi malangizo ofotokozedwa bwino, ofunikira pa kuchita bwino kwanu. Bishop Dag Heward-Mills akutenga kuchokera mukukhala kwake kwa zaka zoposera makumi atatu ngati m’busa, kugawana nafe zinthu zochita mu ntchio ya utumiki. Ngati mwasirira kukhala m’busa wa anthu a Mulungu, iri ndi bukhu loku
Also check out some similar keyword tags authors have used: